Salimo 50:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwe umadana ndi malangizo,*+Ndipo umaponya mawu anga kunkhongo.+ Zekariya 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma iwo anakanabe kumvetsera.+ Anapitiriza kumulozetsa nkhongo+ ndipo anatseka makutu awo kuti asamve chilichonse.+ Yohane 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Amene amachita zinthu zoipa+ amadana ndi kuwala ndipo safika pamene pali kuwala, kuti ntchito zake zisadzudzulidwe.+
11 Koma iwo anakanabe kumvetsera.+ Anapitiriza kumulozetsa nkhongo+ ndipo anatseka makutu awo kuti asamve chilichonse.+
20 Amene amachita zinthu zoipa+ amadana ndi kuwala ndipo safika pamene pali kuwala, kuti ntchito zake zisadzudzulidwe.+