Genesis 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo iwo anati: “Choka apa!” Ananenanso kuti: “Uyu ndi wobwera kwathu kuno, ndipo akukhala monga mlendo.+ Ndiye lero azitiuza zochita?+ Tsopano iweyo tikuchita zoopsa kuposa iwowo.” Atatero iwo anamukhamukira Lotiyo ndi kumupanikiza,+ moti anatsala pang’ono kuthyola chitseko.+ Ezekieli 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndikauza munthu woipa kuti, ‘Munthu woipa iwe, udzafa ndithu,’+ koma iwe osanena mawu alionse ochenjeza woipayo kuti asiye njira yake,+ iyeyo poti ndi woipa adzafa chifukwa cha zolakwa zake,+ koma magazi ake ndidzawafuna kuchokera m’manja mwako.
9 Pamenepo iwo anati: “Choka apa!” Ananenanso kuti: “Uyu ndi wobwera kwathu kuno, ndipo akukhala monga mlendo.+ Ndiye lero azitiuza zochita?+ Tsopano iweyo tikuchita zoopsa kuposa iwowo.” Atatero iwo anamukhamukira Lotiyo ndi kumupanikiza,+ moti anatsala pang’ono kuthyola chitseko.+
8 Ndikauza munthu woipa kuti, ‘Munthu woipa iwe, udzafa ndithu,’+ koma iwe osanena mawu alionse ochenjeza woipayo kuti asiye njira yake,+ iyeyo poti ndi woipa adzafa chifukwa cha zolakwa zake,+ koma magazi ake ndidzawafuna kuchokera m’manja mwako.