Numeri 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Akaziwo ankabwera kudzaitana Aisiraeliwo kuti azipita nawo limodzi kokapereka nsembe kwa milungu yawo.+ Kumeneko, Aisiraeliwo ankadya ndi kugwadira milungu ya Amowabuwo.+ 1 Akorinto 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano zinthu zimenezi zinakhala zitsanzo kwa ife, kuti ifenso tisakhale anthu olakalaka zinthu zoipa+ ngati mmene iwo anachitira. Yuda 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale zili choncho, anthu amenewanso, pokonda zongolota,+ akuipitsa matupi ndi kunyalanyaza ulamuliro+ ndipo amalankhula zonyoza amene ali ndi ulemerero.+
2 Akaziwo ankabwera kudzaitana Aisiraeliwo kuti azipita nawo limodzi kokapereka nsembe kwa milungu yawo.+ Kumeneko, Aisiraeliwo ankadya ndi kugwadira milungu ya Amowabuwo.+
6 Tsopano zinthu zimenezi zinakhala zitsanzo kwa ife, kuti ifenso tisakhale anthu olakalaka zinthu zoipa+ ngati mmene iwo anachitira.
8 Ngakhale zili choncho, anthu amenewanso, pokonda zongolota,+ akuipitsa matupi ndi kunyalanyaza ulamuliro+ ndipo amalankhula zonyoza amene ali ndi ulemerero.+