Genesis 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa chifukwa chimenechi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake,+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+ Genesis 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+ Mateyu 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anachita zimenezi chifukwa Yohane anali kumuuza kuti: “N’kosaloleka kutenga mkaziyu kuti akhale mkazi wanu.”+
24 Pa chifukwa chimenechi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake,+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+
3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+
4 Anachita zimenezi chifukwa Yohane anali kumuuza kuti: “N’kosaloleka kutenga mkaziyu kuti akhale mkazi wanu.”+