Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 M’kamwa mwake mwadzaza matemberero, chinyengo ndi kupondereza ena.+

      Pansi pa lilime lake pamatuluka mavuto ndi zopweteka ena.+

  • Mateyu 12:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ana a njoka inu,+ mungalankhule bwanji zinthu zabwino, pamene muli oipa?+ Pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+

  • Machitidwe 20:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka+ kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+

  • Yakobo 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Lilimenso ndi moto.+ Mwa ziwalo zathu zonse, lilime ndilo lili lodzaza ndi zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse.+ Lili ndi moto wa Gehena* ndipo limayatsa moyo wonse wa munthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena