Deuteronomo 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chotero mawu angawa muwasunge m’mitima yanu+ ndi kuwatsatira m’moyo wanu. Muwamange monga chizindikiro padzanja lanu, ndipo akhale ngati chomanga pamphumi panu.*+ Miyambo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anzeru ndiwo amapitiriza kuphunzira zinthu zamtengo wapatali,+ koma pakamwa pa wopusa patsala pang’ono kuwonongeka.+
18 “Chotero mawu angawa muwasunge m’mitima yanu+ ndi kuwatsatira m’moyo wanu. Muwamange monga chizindikiro padzanja lanu, ndipo akhale ngati chomanga pamphumi panu.*+
14 Anzeru ndiwo amapitiriza kuphunzira zinthu zamtengo wapatali,+ koma pakamwa pa wopusa patsala pang’ono kuwonongeka.+