Miyambo 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Aliyense wochita chigololo ndi mkazi alibe nzeru mumtima mwake.+ Amene amachita zimenezi amawononga moyo wake.+ Miyambo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Aliyense amene ali wosadziwa zinthu apatukire kuno.”+ Aliyense amene ali wopanda nzeru mumtima mwake,+ mkaziyo wamuuza kuti:
32 Aliyense wochita chigololo ndi mkazi alibe nzeru mumtima mwake.+ Amene amachita zimenezi amawononga moyo wake.+
16 “Aliyense amene ali wosadziwa zinthu apatukire kuno.”+ Aliyense amene ali wopanda nzeru mumtima mwake,+ mkaziyo wamuuza kuti: