Miyambo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti iwo sagona kufikira atachita zoipa.+ Tulo sitiwabwerera mpaka atakhumudwitsa wina.+ Miyambo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 mtima wokonzera ena ziwembu,+ mapazi othamangira kukachita zoipa,+ Miyambo 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiponso, si bwino kuti munthu akhale wosadziwa zinthu,+ ndipo woyenda mofulumira ndi mapazi ake akuchimwa.+
2 Ndiponso, si bwino kuti munthu akhale wosadziwa zinthu,+ ndipo woyenda mofulumira ndi mapazi ake akuchimwa.+