Miyambo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja okhetsa magazi a anthu osalakwa,+ Yesaya 59:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mapazi awo amangothamangira kukachita zoipa,+ ndipo amafulumira kuti akakhetse magazi osalakwa.+ Maganizo awo ndi opweteka anzawo.+ M’misewu mwawo amangokhalira kusakazana ndi kuwonongana.+ Aroma 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mapazi awo amathamangira kukhetsa magazi.”+
7 Mapazi awo amangothamangira kukachita zoipa,+ ndipo amafulumira kuti akakhetse magazi osalakwa.+ Maganizo awo ndi opweteka anzawo.+ M’misewu mwawo amangokhalira kusakazana ndi kuwonongana.+