Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ Miyambo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yothandiza kuti munthu wosadziwa akhale wochenjera,+kuti wachinyamata akhale wodziwa zinthu+ ndiponso kuti azitha kuganiza bwino.+
7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+
4 Yothandiza kuti munthu wosadziwa akhale wochenjera,+kuti wachinyamata akhale wodziwa zinthu+ ndiponso kuti azitha kuganiza bwino.+