Salimo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka. Yesaya 45:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndalumbira pa ine mwini.+ Mawuwo atuluka m’kamwa mwanga m’chilungamo,+ moti sadzabwerera.+ Ndalumbira kuti bondo lililonse lidzagwadira ine+ ndipo lilime lililonse lidzalumbira kwa ine,+
6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka.
23 Ndalumbira pa ine mwini.+ Mawuwo atuluka m’kamwa mwanga m’chilungamo,+ moti sadzabwerera.+ Ndalumbira kuti bondo lililonse lidzagwadira ine+ ndipo lilime lililonse lidzalumbira kwa ine,+