Miyambo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuganiza bwino kudzakuyang’anira,+ ndipo kuzindikira kudzakuteteza,+ Miyambo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kuti uteteze kuganiza bwino,+ ndiponso kuti milomo yako iteteze kudziwa zinthu.+