Genesis 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano Mulungu anatcha mtundawo Dziko,+ koma madzi osonkhanawo anawatcha Nyanja.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.+ Salimo 90:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mapiri asanabadwe,+Kapena musanakhazikitse dziko lapansi+ ndi malo okhalapo anthu,*+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+
10 Tsopano Mulungu anatcha mtundawo Dziko,+ koma madzi osonkhanawo anawatcha Nyanja.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.+
2 Mapiri asanabadwe,+Kapena musanakhazikitse dziko lapansi+ ndi malo okhalapo anthu,*+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+