Genesis 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mulungu tsopano anati: “Pakhale mlengalenga+ pakati pa madzi, ndiponso pakhale cholekanitsa pakati pa madzi ndi madzi.”+ Yobu 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anaika malire ozungulira pamwamba pa madzi,+Kumene kuwala kumakathera mu mdima.
6 Mulungu tsopano anati: “Pakhale mlengalenga+ pakati pa madzi, ndiponso pakhale cholekanitsa pakati pa madzi ndi madzi.”+