Genesis 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Mulungu anati: “Madzi apansi pa thambo asonkhane malo amodzi, mtundanso uonekere.”+ Ndipo zinaterodi.
9 Kenako Mulungu anati: “Madzi apansi pa thambo asonkhane malo amodzi, mtundanso uonekere.”+ Ndipo zinaterodi.