Mateyu 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Odala ndi anthu amene amazindikira zosowa zawo zauzimu,+ chifukwa ufumu wakumwamba ndi wawo.+ 1 Atesalonika 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero tisapitirize kugona+ ngati mmene enawo akuchitira,+ koma tikhalebe maso+ ndipo tikhalebe oganiza bwino.+
6 Chotero tisapitirize kugona+ ngati mmene enawo akuchitira,+ koma tikhalebe maso+ ndipo tikhalebe oganiza bwino.+