Miyambo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu wabwino Yehova amakondwera naye,+ koma munthu wamaganizo oipa iye amamutcha woipa.+ Aefeso 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anatero kuti kukoma mtima kwakukulu kwaulemerero+ kumene anatisonyeza kudzera mwa wokondedwa wake+ kutamandike.+
6 Anatero kuti kukoma mtima kwakukulu kwaulemerero+ kumene anatisonyeza kudzera mwa wokondedwa wake+ kutamandike.+