Luka 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nthawi ya chakudya chamadzulocho itakwana, anatumiza kapolo wake kukauza oitanidwawo kuti, ‘Tiyeni,+ chifukwa zonse zakonzedwa tsopano.’
17 Nthawi ya chakudya chamadzulocho itakwana, anatumiza kapolo wake kukauza oitanidwawo kuti, ‘Tiyeni,+ chifukwa zonse zakonzedwa tsopano.’