Miyambo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mnyamatayo anali kuyenda mumsewu pafupi ndi mphambano yopita kunyumba ya mkazi wachilendo. Iye anali kuyenda panjira yopita kunyumba ya mkaziyo,+ Miyambo 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti mkaziyo waphetsa anthu ambiri,+ ndipo onse amene aphedwa ndi iye ndi ochuluka.+ Miyambo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti hule lili ngati dzenje lakuya,+ ndipo mkazi wachilendo ali ngati chitsime chopapatiza.
8 Mnyamatayo anali kuyenda mumsewu pafupi ndi mphambano yopita kunyumba ya mkazi wachilendo. Iye anali kuyenda panjira yopita kunyumba ya mkaziyo,+