Miyambo 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Bwera tisonyezane chikondi mpaka chitikwane. Tichite zimenezi mpaka m’mawa. Tisangalatsane pouzana mawu achikondi.+ Aefeso 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti zimene iwo amachita mseri n’zochititsa manyazi ngakhale kuzitchula.+
18 Bwera tisonyezane chikondi mpaka chitikwane. Tichite zimenezi mpaka m’mawa. Tisangalatsane pouzana mawu achikondi.+