Miyambo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana amakhala wanzeru ngati akulandira malangizo* kuchokera kwa bambo ake.+ Koma amene sanamve chidzudzulo amakhala wonyoza.+ Miyambo 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Bambo wa munthu wolungama ndithu adzasangalala.+ Bambo wobereka mwana wanzeru adzakondwera naye.+ Miyambo 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwana wanga, khala wanzeru ndi kukondweretsa mtima wanga,+ kuti ndimuyankhe amene akunditonza.+ Miyambo 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthu wokonda nzeru amasangalatsa bambo ake,+ koma woyenda ndi mahule amawononga zinthu zamtengo wapatali.+
13 Mwana amakhala wanzeru ngati akulandira malangizo* kuchokera kwa bambo ake.+ Koma amene sanamve chidzudzulo amakhala wonyoza.+
3 Munthu wokonda nzeru amasangalatsa bambo ake,+ koma woyenda ndi mahule amawononga zinthu zamtengo wapatali.+