Miyambo 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Wa mtima wopotoka sadzapeza zabwino,+ ndipo wa lilime lokhota adzagwera m’tsoka.+ Miyambo 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Milomo ya munthu wopusa imalowa mu mkangano,+ ndipo pakamwa pake pamaitana zikwapu.+ Mlaliki 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mawu a m’kamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamuwononga.+
12 Mawu a m’kamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamuwononga.+