Miyambo 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zipatso za munthu wolungama ndizo mtengo wa moyo,+ ndipo munthu wopulumutsa miyoyo ndi wanzeru.+ Habakuku 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Taona! Iye wadzitukumula+ ndipo si wowongoka mtima. Koma wolungama adzakhalabe ndi moyo mwa chikhulupiriro chake.+ Agalatiya 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti amene akufesa ndi cholinga chopindulitsa thupi lake, adzakolola chiwonongeko kuchokera m’thupi lakelo,+ koma amene akutsatira mzimu wa Mulungu+ adzakolola moyo wosatha kuchokera ku mzimuwo.+
4 “Taona! Iye wadzitukumula+ ndipo si wowongoka mtima. Koma wolungama adzakhalabe ndi moyo mwa chikhulupiriro chake.+
8 Pakuti amene akufesa ndi cholinga chopindulitsa thupi lake, adzakolola chiwonongeko kuchokera m’thupi lakelo,+ koma amene akutsatira mzimu wa Mulungu+ adzakolola moyo wosatha kuchokera ku mzimuwo.+