Salimo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+ Salimo 125:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 125 Okhulupirira Yehova+Ali ngati phiri la Ziyoni,+ limene silingagwedezeke, koma lidzakhalapo mpaka kalekale.+
8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+
125 Okhulupirira Yehova+Ali ngati phiri la Ziyoni,+ limene silingagwedezeke, koma lidzakhalapo mpaka kalekale.+