Salimo 63:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo mfumu idzakondwera mwa Mulungu.+Aliyense wolumbira m’dzina la Mulungu adzam’tamanda,+Pakuti pakamwa pa anthu olankhula chinyengo padzatsekedwa.+
11 Ndipo mfumu idzakondwera mwa Mulungu.+Aliyense wolumbira m’dzina la Mulungu adzam’tamanda,+Pakuti pakamwa pa anthu olankhula chinyengo padzatsekedwa.+