Miyambo 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kulanda zinthu za ena kumene anthu oipa amachita n’kumene kudzawawononge,+ chifukwa akana kuchita chilungamo.+ Miyambo 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Woyenda mosalakwa adzapulumutsidwa,+ koma woyenda m’njira zokhota adzagwa mwadzidzidzi.+ Yesaya 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kuwonongeka kwa opanduka ndi kwa ochimwa kudzachitikira limodzi,+ ndipo anthu omusiya Yehova adzatha.+
7 Kulanda zinthu za ena kumene anthu oipa amachita n’kumene kudzawawononge,+ chifukwa akana kuchita chilungamo.+
28 Kuwonongeka kwa opanduka ndi kwa ochimwa kudzachitikira limodzi,+ ndipo anthu omusiya Yehova adzatha.+