Yesaya 54:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+ Mateyu 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 pakuti wolankhula simudzakhala inu panokha, koma mzimu wa Atate wanu udzalankhula kudzera mwa inu.+ Yohane 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zinalembedwa m’Mabuku a Aneneri kuti, ‘Ndipo onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.+
13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+
20 pakuti wolankhula simudzakhala inu panokha, koma mzimu wa Atate wanu udzalankhula kudzera mwa inu.+
45 Zinalembedwa m’Mabuku a Aneneri kuti, ‘Ndipo onse adzaphunzitsidwa ndi Yehova.’*+ Aliyense amene wamva kwa Atate ndipo waphunzira amabwera kwa ine.+