Genesis 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pambuyo pake Yehova anauza Nowa kuti: “Lowa m’chingalawacho, iwe ndi banja lako,+ chifukwa iwe ndi amene ndakuona kuti ndiwe wolungama pakati pa m’badwo uwu.+ Miyambo 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 M’njira yachilungamo muli moyo,+ ndipo ulendo wa m’njira imeneyi suthera ku imfa.+ Miyambo 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Woipa adzakankhidwa chifukwa cha kuipa kwake,+ koma wolungama adzapeza malo othawirako chifukwa cha mtima wake wosagawanika.+
7 Pambuyo pake Yehova anauza Nowa kuti: “Lowa m’chingalawacho, iwe ndi banja lako,+ chifukwa iwe ndi amene ndakuona kuti ndiwe wolungama pakati pa m’badwo uwu.+
32 Woipa adzakankhidwa chifukwa cha kuipa kwake,+ koma wolungama adzapeza malo othawirako chifukwa cha mtima wake wosagawanika.+