Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Haribona,+ mmodzi mwa nduna za panyumba ya mfumu+ amene anali pamaso pa mfumu anati: “Palinso mtengo+ umene Hamani anapangira Moredekai, amene analankhula zabwino za mfumu.+ Mtengowu uli m’nyumba ya Hamani ndipo ndi wotalika mikono 50.” Pamenepo mfumu inati: “Amuna inu, kam’pachikeni pamtengo umenewo.”+

  • Miyambo 21:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Munthu woipa ndiye dipo la wolungama,+ ndipo munthu wochita zachinyengo amalowa m’malo mwa anthu owongoka mtima.+

  • Danieli 6:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Zitatero, mfumu inalamula kuti abweretse amuna amphamvu amene ananenera Danieli zoipa aja,+ ndipo anawabweretsadi. Kenako anawaponya m’dzenje la mikango+ pamodzi ndi ana awo ndi akazi awo.+ Iwo asanafike n’komwe pansi pa dzenjelo, mikango inawakhadzulakhadzula ndi kuphwanya mafupa awo onse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena