Miyambo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nzeru zikalowa mumtima mwako,+ ndipo kudziwa zinthu kukakhala kosangalatsa m’moyo wako,+ Miyambo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kuopa Yehova ndiko chiyambi cha nzeru.+ Kudziwa Woyera Koposa, ndiko kumvetsa zinthu.+