Miyambo 14:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Chilungamo chimakweza mtundu wa anthu,+ koma tchimo limachititsa manyazi mitundu ya anthu.+ Miyambo 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu olankhula modzitama amabutsa mkwiyo wa mzinda,+ koma anthu anzeru amaletsa mkwiyo.+