Miyambo 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zolingalira sizikwaniritsidwa ngati anthu sakambirana moona mtima,+ koma aphungu akachuluka zimakwaniritsidwa.+ Miyambo 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+ Miyambo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+
22 Zolingalira sizikwaniritsidwa ngati anthu sakambirana moona mtima,+ koma aphungu akachuluka zimakwaniritsidwa.+
18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+
6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+