Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ndiyeno Davide anamva kuti Nabala wamwalira. Atatero, iye anati: “Adalitsike Yehova amene wandiweruzira mlandu+ ndi kundimasula ku chitonzo+ cha Nabala, komanso wagwira ine mtumiki wake kuti ndisachite choipa.+ Yehova wabwezera zoipa za Nabala pamutu pake!”+ Pamenepo Davide anatumiza anthu kuti akamufunsirire Abigayeli, kuti akhale mkazi wake.+

  • Miyambo 31:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Chikoka chikhoza kukhala chachinyengo+ ndipo kukongola kukhoza kukhala kopanda phindu,+ koma mkazi woopa Yehova ndi amene amatamandidwa chifukwa cha zochita zake.+

  • 1 Timoteyo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mofanana ndi zimenezi, ndikufunanso kuti akazi azidzikongoletsa ndi zovala zoyenera, povala mwaulemu+ ndi mwanzeru, osati kudzikongoletsa ndi masitayilo omangira tsitsi, golide, ngale, kapena zovala zamtengo wapatali.+

  • 1 Petulo 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma kukhale kwa munthu wobisika+ wamumtima, atavala zovala zosawonongeka,+ ndizo mzimu wabata ndi wofatsa+ umene uli wamtengo wapatali pamaso pa Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena