Yobu 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gawo la munthu woipa lochokera kwa Mulungu,+Zomwe adzalandire kwa Wamphamvuyonse monga cholowa cha ozunza anzawo, ndi izi: Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+
13 Gawo la munthu woipa lochokera kwa Mulungu,+Zomwe adzalandire kwa Wamphamvuyonse monga cholowa cha ozunza anzawo, ndi izi: