Miyambo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gwira malangizo,+ usawataye.+ Uwasunge bwino chifukwa iwo ndiwo moyo wako.+ Yeremiya 39:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Pakuti ine ndidzakupulumutsa ndithu, ndipo sudzaphedwa ndi lupanga, koma udzapulumutsa moyo wako+ chifukwa chakuti wandikhulupirira,’+ watero Yehova.”
18 “‘Pakuti ine ndidzakupulumutsa ndithu, ndipo sudzaphedwa ndi lupanga, koma udzapulumutsa moyo wako+ chifukwa chakuti wandikhulupirira,’+ watero Yehova.”