Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “‘Munthu wolungama akasiya chilungamo chake n’kumachita zinthu zopanda chilungamo,+ akamachita zopanda chilungamo+ n’kumakhalabe ndi moyo, zinthu zolungama zonse zimene anachita sizidzakumbukiridwa.+ Iye adzafa chifukwa chochita zinthu mosakhulupirika ndiponso chifukwa cha machimo ake amene anachita.+

  • Ezekieli 33:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma iweyo ukachenjeza munthu woipa kuti asiye njira zake ndi kubwerera, koma iye osasiya njira zake zoipa ndi kubwerera, munthuyo adzafa chifukwa cha zoipa zake.+ Koma iweyo udzapulumutsa moyo wako.+

  • 2 Atesalonika 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chiweruzo cha Mulunguchi n’cholungama chifukwa akubwezera masautso kwa amene amakusautsani.+

  • 1 Petulo 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Ndipo ngati munthu wolungama adzapulumuka movutikira,+ kodi munthu wosaopa Mulungu ndi wochimwa adzaoneka n’komwe?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena