Salimo 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtima wanga wosagawanika ndiponso wowongoka unditeteze,+Pakuti chiyembekezo changa chili mwa inu.+ Miyambo 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Palibe chopweteka chimene chidzagwere wolungama,+ koma anthu oipa ndi amene tsoka lizidzangowagwera.+ Miyambo 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 M’njira yachilungamo muli moyo,+ ndipo ulendo wa m’njira imeneyi suthera ku imfa.+
21 Mtima wanga wosagawanika ndiponso wowongoka unditeteze,+Pakuti chiyembekezo changa chili mwa inu.+
21 Palibe chopweteka chimene chidzagwere wolungama,+ koma anthu oipa ndi amene tsoka lizidzangowagwera.+