-
Genesis 21:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Anapitiriza kunena kuti: “Akanadziwa ndani kuti Sara adzayamwitsa mwana, moti n’kumuuza Abulahamu zimenezo? Koma taonani, ndamuberekera mwana Abulahamu atakalamba.”
-