Genesis 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ukasintha n’kuchita chabwino, sindikuyanja kodi?+ Koma ngati susintha kuti uchite chabwino, uchimo wamyata pakhomo kukudikirira, ndipo ukulakalaka kukudya.+ Kodi iweyo suugonjetsa?”+ Deuteronomo 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Yehova adzakutumizira matemberero,+ chisokonezo+ ndi chilango+ pa ntchito zako zonse zimene ukuyesa kugwira. Adzakuchitira zimenezi kufikira utafafanizidwa ndi kutha mofulumira, chifukwa cha kuipa kwa zochita zako popeza kuti wandisiya.+
7 Ukasintha n’kuchita chabwino, sindikuyanja kodi?+ Koma ngati susintha kuti uchite chabwino, uchimo wamyata pakhomo kukudikirira, ndipo ukulakalaka kukudya.+ Kodi iweyo suugonjetsa?”+
20 “Yehova adzakutumizira matemberero,+ chisokonezo+ ndi chilango+ pa ntchito zako zonse zimene ukuyesa kugwira. Adzakuchitira zimenezi kufikira utafafanizidwa ndi kutha mofulumira, chifukwa cha kuipa kwa zochita zako popeza kuti wandisiya.+