1 Mafumu 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Mulungu anamuuza kuti: “Popeza wapempha zimenezi ndipo sunapemphe masiku ambiri, chuma,+ kapena moyo wa adani ako, koma wapempha kuti ukhale womvetsa zinthu kuti uzitha kuweruza milandu,+ Miyambo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kuopa Yehova ndiko chiyambi cha nzeru.+ Kudziwa Woyera Koposa, ndiko kumvetsa zinthu.+ Miyambo 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mtima wa munthu womvetsa zinthu umadziwa zinthu,+ ndipo khutu la anzeru limafunafuna kudziwa zinthu.+
11 Ndiyeno Mulungu anamuuza kuti: “Popeza wapempha zimenezi ndipo sunapemphe masiku ambiri, chuma,+ kapena moyo wa adani ako, koma wapempha kuti ukhale womvetsa zinthu kuti uzitha kuweruza milandu,+
15 Mtima wa munthu womvetsa zinthu umadziwa zinthu,+ ndipo khutu la anzeru limafunafuna kudziwa zinthu.+