Miyambo 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 koma wolephera kundipeza akupweteka moyo wake.+ Onse odana ndi ine ndiye kuti amakonda imfa.”+ Miyambo 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Um’kwapule ndi chikwapu, kuti upulumutse moyo wake ku Manda.+