Deuteronomo 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “M’thumba lako, usakhale ndi miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu,+ usakhale ndi muyezo waukulu ndi wina waung’ono. Miyambo 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu ndiponso miyezo iwiri yosiyana ya efa,*+ zonsezi n’zonyansa kwa Yehova.+ Mika 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi ndingakhale woyera ndili ndi sikelo yachinyengo, ndiponso thumba lachinyengo lamiyala yoyezera zinthu?+
13 “M’thumba lako, usakhale ndi miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu,+ usakhale ndi muyezo waukulu ndi wina waung’ono.
10 Miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu ndiponso miyezo iwiri yosiyana ya efa,*+ zonsezi n’zonyansa kwa Yehova.+
11 Kodi ndingakhale woyera ndili ndi sikelo yachinyengo, ndiponso thumba lachinyengo lamiyala yoyezera zinthu?+