Salimo 101:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Maso anga ali pa okhulupirika a padziko lapansi,+Kuti akhale ndi ine.+Woyenda m’njira yowongoka,+Ndi amene adzanditumikira.+
6 Maso anga ali pa okhulupirika a padziko lapansi,+Kuti akhale ndi ine.+Woyenda m’njira yowongoka,+Ndi amene adzanditumikira.+