1 Mafumu 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 taona, ndichita mogwirizanadi ndi mawu ako.+ Ndithu ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ moti ndi kale lonse sipanakhalepo munthu ngati iwe, ndipo pambuyo pako sipadzakhalanso wina ngati iwe.+ Miyambo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nzeru ndiyo chinthu chofunika kwambiri.+ Peza nzeru, ndipo pa zinthu zonse zimene upeze, upezenso luso lomvetsa zinthu.+ Aroma 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti anthu onse+ adziwa kuti ndinu omvera. Choncho ndikusangalala chifukwa cha inu. Koma ndikufuna kuti mukhale anzeru+ pa zinthu zabwino, ndi osadziwa+ kanthu pa zinthu zoipa.+
12 taona, ndichita mogwirizanadi ndi mawu ako.+ Ndithu ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ moti ndi kale lonse sipanakhalepo munthu ngati iwe, ndipo pambuyo pako sipadzakhalanso wina ngati iwe.+
7 Nzeru ndiyo chinthu chofunika kwambiri.+ Peza nzeru, ndipo pa zinthu zonse zimene upeze, upezenso luso lomvetsa zinthu.+
19 Pakuti anthu onse+ adziwa kuti ndinu omvera. Choncho ndikusangalala chifukwa cha inu. Koma ndikufuna kuti mukhale anzeru+ pa zinthu zabwino, ndi osadziwa+ kanthu pa zinthu zoipa.+