Yobu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi inuyo simwam’tchinga iyeyo?+ Mwatchingiranso nyumba yake ndi chilichonse chimene ali nacho. Mwadalitsa ntchito ya manja ake+ ndipo ziweto zake zachuluka kwambiri padziko lapansi. Salimo 41:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma ine mwandichirikiza chifukwa cha mtima wanga wosagawanika,+Ndipo mudzandiika pamaso panu mpaka kalekale.+ Miyambo 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Woyenda mosalakwa adzapulumutsidwa,+ koma woyenda m’njira zokhota adzagwa mwadzidzidzi.+
10 Kodi inuyo simwam’tchinga iyeyo?+ Mwatchingiranso nyumba yake ndi chilichonse chimene ali nacho. Mwadalitsa ntchito ya manja ake+ ndipo ziweto zake zachuluka kwambiri padziko lapansi.
12 Koma ine mwandichirikiza chifukwa cha mtima wanga wosagawanika,+Ndipo mudzandiika pamaso panu mpaka kalekale.+