Miyambo 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba,+ kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+ Miyambo 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuli bwino kukhala m’chipululu kusiyana ndi kukhala mokhumudwa ndi mkazi wolongolola.+
9 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba,+ kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+