Salimo 141:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musachititse mtima wanga kukonda choipa chilichonse,+Kuti ndisamachite zinthu zoipa zonditchukitsa,+Pamodzi ndi amene amachita zinthu zopweteka anzawo,+Kuti ndisadye chakudya chawo chapamwamba.+
4 Musachititse mtima wanga kukonda choipa chilichonse,+Kuti ndisamachite zinthu zoipa zonditchukitsa,+Pamodzi ndi amene amachita zinthu zopweteka anzawo,+Kuti ndisadye chakudya chawo chapamwamba.+