Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 32:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mukamuuzenso kuti, ‘Ndiponso kapolo wanu Yakobo ali m’mbuyo mwathumu.’”+ Popeza mumtima mwake anati: “Mwina ndingamusangalatse potsogoza mphatsoyi,+ ndipo pambuyo pake ndingathe kuonana naye pamasom’pamaso, kuti mwina angandilandire bwino.”+

  • Genesis 43:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno bambo awo Isiraeli anawauza kuti: “Chabwino, ngati ndi choncho,+ chitani izi: Tengani zinthu zamtengo wapatali za dziko lino m’matumba anu, mukam’patse munthuyo monga mphatso.+ Tengani mafuta a basamu+ pang’ono, uchi+ pang’ono, mafuta onunkhira a labidanamu, khungwa la utomoni wonunkhira,+ mtedza wa pisitasho, ndi zipatso za amondi.+

  • Miyambo 17:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mphatso ndiyo mwala wamtengo wapatali m’maso mwa mwiniwake wolemekezeka.+ Kulikonse kumene amapita zinthu zimamuyendera bwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena