2 Samueli 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano mfumu inafunsa kuti: “Kodi mwana wa mbuye wako ali kuti?”+ Pamenepo Ziba anauza mfumu kuti: “Watsalira ku Yerusalemu, pakuti wanena kuti, ‘Lero nyumba ya Isiraeli indibwezera ufumu wa bambo anga.’”+
3 Tsopano mfumu inafunsa kuti: “Kodi mwana wa mbuye wako ali kuti?”+ Pamenepo Ziba anauza mfumu kuti: “Watsalira ku Yerusalemu, pakuti wanena kuti, ‘Lero nyumba ya Isiraeli indibwezera ufumu wa bambo anga.’”+