Genesis 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Masiku onse amene dziko lapansi lidzakhalapo, kubzala mbewu ndi kukolola sikudzatha. Ndiponso, nyengo yozizira ndi yotentha, chilimwe ndi chisanu, usana ndi usiku, zidzakhalapobe.”+ Salimo 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Limatuluka kuchokera kumalekezero ena a kumwamba,Ndi kuzungulira mpaka kumalekezero enanso.+Palibe chinthu chilichonse chimene sichimva kutentha kwake.+
22 Masiku onse amene dziko lapansi lidzakhalapo, kubzala mbewu ndi kukolola sikudzatha. Ndiponso, nyengo yozizira ndi yotentha, chilimwe ndi chisanu, usana ndi usiku, zidzakhalapobe.”+
6 Limatuluka kuchokera kumalekezero ena a kumwamba,Ndi kuzungulira mpaka kumalekezero enanso.+Palibe chinthu chilichonse chimene sichimva kutentha kwake.+